-
Yoswa 19:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Kenako anabwerera kulowera kumʼmawa ku Beti-dagoni, nʼkukafika ku Zebuloni ndi kumpoto kwa chigwa cha Ifita-eli. Anakafikanso ku Beti-emeki ndi ku Nehieli nʼkupitirira mpaka ku Kabulu chakumanzere.
-