Yoswa 19:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kenako anakhota n’kubwerera kulowera kotulukira dzuwa ku Beti-dagoni, n’kukafika ku Zebuloni+ ndi kumpoto kwa chigwa cha Ifita-eli. Anakafikanso ku Beti-emeki ndi ku Nehieli n’kupitirira mpaka ku Kabulu chakumanzere.
27 Kenako anakhota n’kubwerera kulowera kotulukira dzuwa ku Beti-dagoni, n’kukafika ku Zebuloni+ ndi kumpoto kwa chigwa cha Ifita-eli. Anakafikanso ku Beti-emeki ndi ku Nehieli n’kupitirira mpaka ku Kabulu chakumanzere.