Yoswa 24:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Yehova anathamangitsa mitundu yonse ya anthu+ pamaso pathu, ngakhale Aamori amene anali kukhala m’dzikoli. Choncho, nafenso tizitumikira Yehova chifukwa iye ndi Mulungu wathu.”+
18 Yehova anathamangitsa mitundu yonse ya anthu+ pamaso pathu, ngakhale Aamori amene anali kukhala m’dzikoli. Choncho, nafenso tizitumikira Yehova chifukwa iye ndi Mulungu wathu.”+