Yoswa 24:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Kenako Yoswa analemba mawu amenewa mʼbuku la Chilamulo cha Mulungu.+ Atatero anatenga mwala waukulu+ ndi kuuika pansi pa mtengo waukulu kwambiri umene uli pafupi ndi malo opatulika a Yehova.
26 Kenako Yoswa analemba mawu amenewa mʼbuku la Chilamulo cha Mulungu.+ Atatero anatenga mwala waukulu+ ndi kuuika pansi pa mtengo waukulu kwambiri umene uli pafupi ndi malo opatulika a Yehova.