Yoswa 24:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndiyeno Yoswa analemba mawu amenewa m’buku la chilamulo cha Mulungu.+ Atatero, anatenga mwala waukulu+ ndi kuuika pansi pa mtengo waukulu kwambiri+ umene uli pafupi ndi malo opatulika a Yehova.
26 Ndiyeno Yoswa analemba mawu amenewa m’buku la chilamulo cha Mulungu.+ Atatero, anatenga mwala waukulu+ ndi kuuika pansi pa mtengo waukulu kwambiri+ umene uli pafupi ndi malo opatulika a Yehova.