Yoswa 24:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Aisiraeli anapitiriza kutumikira Yehova masiku onse amene Yoswa anali ndi moyo komanso masiku onse a akulu amene anakhalabe ndi moyo Yoswa atamwalira, omwe ankadziwa zinthu zonse zimene Yehova anachitira Aisiraeli.+
31 Aisiraeli anapitiriza kutumikira Yehova masiku onse amene Yoswa anali ndi moyo komanso masiku onse a akulu amene anakhalabe ndi moyo Yoswa atamwalira, omwe ankadziwa zinthu zonse zimene Yehova anachitira Aisiraeli.+