Oweruza 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iwo anati: “Ine ndinkaganiza kuti unadana naye,+ choncho ndinamʼpereka kwa mmodzi wa anyamata amene ankakhala nawe aja.+ Mngʼono wakeyu ndi wokongola kuposa iyeyu. Bwanji utenge ameneyu mʼmalomwake?”
2 Iwo anati: “Ine ndinkaganiza kuti unadana naye,+ choncho ndinamʼpereka kwa mmodzi wa anyamata amene ankakhala nawe aja.+ Mngʼono wakeyu ndi wokongola kuposa iyeyu. Bwanji utenge ameneyu mʼmalomwake?”