-
Oweruza 15:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Choncho Samisoni ananyamuka nʼkukagwira nkhandwe 300. Kenako anatenga nkhandwezo ziwiriziwiri nʼkuzimanga michira. Atatero, anaika muuni umodzi pakati pa michira iwiriyo.
-