-
Oweruza 15:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Zitatero, Afilisiti anafunsa kuti: “Wachita zimenezi ndi ndani?” Ndiyeno anauzidwa kuti: “Ndi Samisoni, mkamwini wa munthu wa ku Timuna uja, chifukwa munthuyu anatenga mkazi wa Samisoni nʼkumupereka kwa mmodzi mwa anyamata amene ankakhala ndi Samisoni ngati anzake a mkwati.”+ Afilisiti atamva zimenezi anapita kukatentha ndi moto mtsikanayo pamodzi ndi bambo ake.+
-