Oweruza 15:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Patapita nthawi, Afilisiti anabwera nʼkumanga msasa ku Yuda ndipo ankayendayenda ku Lehi.+