Oweruza 15:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno anthu a ku Yuda anawafunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani mwabwera kudzatiukira?” Iwo anayankha kuti: “Tabwera kudzagwira* Samisoni kuti timʼchite zimene iye watichitira.”
10 Ndiyeno anthu a ku Yuda anawafunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani mwabwera kudzatiukira?” Iwo anayankha kuti: “Tabwera kudzagwira* Samisoni kuti timʼchite zimene iye watichitira.”