Oweruza 15:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma iwo anamuuza kuti: “Tabwera kudzakugwira* kuti tikakupereke kwa Afilisiti.” Samisoni anayankha kuti: “Lumbirani kuti inuyo simundichitira chilichonse choipa.”
12 Koma iwo anamuuza kuti: “Tabwera kudzakugwira* kuti tikakupereke kwa Afilisiti.” Samisoni anayankha kuti: “Lumbirani kuti inuyo simundichitira chilichonse choipa.”