-
Oweruza 15:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Iwo anamuyankha kuti: “Ayi, sitikupha. Tingokumanga nʼkukakupereka kwa iwowo.”
Choncho anamʼmanga ndi zingwe ziwiri zatsopano nʼkumʼtulutsa kuphangako.
-