Oweruza 15:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Zitatero, anapeza fupa laliwisi la nsagwada za bulu wamphongo ndipo analitenga nʼkupha nalo amuna 1,000.+
15 Zitatero, anapeza fupa laliwisi la nsagwada za bulu wamphongo ndipo analitenga nʼkupha nalo amuna 1,000.+