Oweruza 15:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Atamaliza kulankhula zimenezi, anataya fupalo ndipo malowo anawapatsa dzina lakuti Ramati-lehi.*+