Oweruza 15:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Choncho Mulungu anangʼamba nthaka ku Lehi ndipo panayamba kutuluka madzi.+ Samisoni atamwa madziwo, ludzu lake linatha ndipo anapezanso mphamvu. Nʼchifukwa chake anapatsa malowo dzina lakuti Eni-hakore.* Malo amenewa ali ku Lehi mpaka lero. Oweruza Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:19 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),9/2023, tsa. 4
19 Choncho Mulungu anangʼamba nthaka ku Lehi ndipo panayamba kutuluka madzi.+ Samisoni atamwa madziwo, ludzu lake linatha ndipo anapezanso mphamvu. Nʼchifukwa chake anapatsa malowo dzina lakuti Eni-hakore.* Malo amenewa ali ku Lehi mpaka lero.