-
Oweruza 18:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Iwo anayankha kuti: “Tiyeni tipite tikamenyane nawo, chifukwa ife taona kuti malowo ndi abwino kwambiri. Tisazengereze. Musachedwe, tiyeni tipite tikatenge malowo kuti akhale athu.
-