Oweruza 18:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Poyankha iwo anati: “Nyamukani, tiyeni tipite kukamenyana nawo, chifukwa ife taliona dzikolo ndipo ndi labwino kwambiri.+ Mukuzengerezatu. Musachite ulesi, koma nyamukani mukatenge dzikolo kukhala lanu.+
9 Poyankha iwo anati: “Nyamukani, tiyeni tipite kukamenyana nawo, chifukwa ife taliona dzikolo ndipo ndi labwino kwambiri.+ Mukuzengerezatu. Musachite ulesi, koma nyamukani mukatenge dzikolo kukhala lanu.+