-
1 Samueli 1:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Ndiyeno Elikana mwamuna wake anati: “Hana, nʼchifukwa chiyani ukulira, ndipo nʼchifukwa chiyani sukudya? Komanso nʼchifukwa chiyani wakhumudwa chonchi? Kodi sindikuposa ana aamuna 10 kwa iwe?”
-