1 Samueli 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma Hana anayankha kuti: “Ayi mbuyanga! Munthune ndili ndi nkhawa kwambiri. Sindinamwe vinyo kapena chakumwa chilichonse choledzeretsa, koma ndikufotokozera Yehova nkhawa zanga zonse.+ 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:15 Nsanja ya Olonda,3/15/2007, tsa. 162/1/2001, ptsa. 20-21
15 Koma Hana anayankha kuti: “Ayi mbuyanga! Munthune ndili ndi nkhawa kwambiri. Sindinamwe vinyo kapena chakumwa chilichonse choledzeretsa, koma ndikufotokozera Yehova nkhawa zanga zonse.+