1 Samueli 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chaka chisanathe, Hana anatenga pakati nʼkubereka mwana wamwamuna ndipo anamupatsa dzina+ lakuti Samueli* chifukwa anati, “ndinamupempha kwa Yehova.”
20 Chaka chisanathe, Hana anatenga pakati nʼkubereka mwana wamwamuna ndipo anamupatsa dzina+ lakuti Samueli* chifukwa anati, “ndinamupempha kwa Yehova.”