Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 5:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Mwanayo anamupatsa dzina lakuti Nowa,*+ ndipo anati: “Uyu ndi amene adzatibweretsere mpumulo ku ntchito yathu yovuta komanso yopweteketsa manja, chifukwa cholima nthaka imene Yehova anaitemberera.”+

  • Genesis 41:51
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 51 Mwana woyambayo, Yosefe anamupatsa dzina lakuti Manase*+ chifukwa anati, “Mulungu wandiiwalitsa mavuto anga onse ndi nyumba yonse ya bambo anga.”

  • Ekisodo 2:21, 22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Zitatero Mose anavomereza kukhala ndi Reueli, ndipo iye anapereka Zipora+ mwana wake wamkazi kwa Mose kuti akhale mkazi wake. 22 Kenako Zipora anabereka mwana wamwamuna ndipo Mose anamʼpatsa dzina lakuti Gerisomu,*+ chifukwa anati, “Ndakhala mlendo mʼdziko lachilendo.”+

  • Mateyu 1:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Iye adzabereka mwana wamwamuna ndipo udzamupatse dzina lakuti Yesu,*+ chifukwa adzapulumutsa anthu ake ku machimo awo.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena