1 Samueli 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma Hana sanapite nawo,+ chifukwa anali atauza mwamuna wake kuti: “Mwanayu akadzangosiya kuyamwa, ndidzapita naye. Kenako adzaonekera pamaso pa Yehova ndipo azikakhala komweko.”+ 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:22 Nsanja ya Olonda,3/15/2007, tsa. 16
22 Koma Hana sanapite nawo,+ chifukwa anali atauza mwamuna wake kuti: “Mwanayu akadzangosiya kuyamwa, ndidzapita naye. Kenako adzaonekera pamaso pa Yehova ndipo azikakhala komweko.”+