-
2 Mbiri 31:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Kuwonjezera pamenepo, ankagawiranso amuna oyambira zaka zitatu kupita mʼtsogolo amene anali pamndandanda wa mayina wotsatira makolo awo. Amuna amenewa ankabwera tsiku ndi tsiku kudzatumikira kunyumba ya Yehova komanso kudzagwira ntchito ya magulu awo.
-