-
1 Samueli 1:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Elikana anamuuza kuti: “Chita zimene ukuona kuti nʼzabwino kwa iweyo. Ukhoza kukhala mpaka mwanayo atasiya kuyamwa. Yehova akwaniritse zimene iwe wanena.” Choncho Hana anakhalabe pakhomo ndipo anapitiriza kulera mwana wakeyo mpaka atasiya kuyamwa.
-