1 Samueli 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Musamalankhule modzikweza,Pakamwa panu pasatuluke mawu odzikuza,Chifukwa Yehova ndi Mulungu wodziwa zonse,+Ndipo zochita za anthu, iye amaziyeza molondola.
3 Musamalankhule modzikweza,Pakamwa panu pasatuluke mawu odzikuza,Chifukwa Yehova ndi Mulungu wodziwa zonse,+Ndipo zochita za anthu, iye amaziyeza molondola.