1 Samueli 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Musalankhule modzikweza kwambiri anthu inu,Pakamwa panu pasatuluke mawu odzikuza,+Pakuti Yehova ndi Mulungu wodziwa zonse.+Ndipo zochita za anthu, iye amaziyeza molondola.+
3 Musalankhule modzikweza kwambiri anthu inu,Pakamwa panu pasatuluke mawu odzikuza,+Pakuti Yehova ndi Mulungu wodziwa zonse.+Ndipo zochita za anthu, iye amaziyeza molondola.+