1 Samueli 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Komanso munthu wopereka nsembe asanapsereze mafuta,+ mtumiki wa wansembe ankabwera nʼkumuuza kuti: “Ndipatse nyama yosaphika ndikawotchere wansembe. Wansembe sakufuna nyama yophika koma yosaphika.”
15 Komanso munthu wopereka nsembe asanapsereze mafuta,+ mtumiki wa wansembe ankabwera nʼkumuuza kuti: “Ndipatse nyama yosaphika ndikawotchere wansembe. Wansembe sakufuna nyama yophika koma yosaphika.”