1 Samueli 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Komanso, asanapsereze mafuta,+ mtumiki wa wansembe anali kubwera kudzauza munthu wopereka nsembeyo kuti: “Ndipatse nyama yaiwisi kuti ndikamuwotchere wansembe, kuti wansembe asalandire nyama yophika koma yaiwisi.”+
15 Komanso, asanapsereze mafuta,+ mtumiki wa wansembe anali kubwera kudzauza munthu wopereka nsembeyo kuti: “Ndipatse nyama yaiwisi kuti ndikamuwotchere wansembe, kuti wansembe asalandire nyama yophika koma yaiwisi.”+