1 Samueli 2:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Munthu akachimwira mnzake, munthu wina akhoza kumuchonderera kwa Yehova,* koma akachimwira Yehova,+ angamupempherere ndi ndani?” Koma anawo sankamvera bambo awo ndipo tsopano Yehova anali atatsimikiza mtima kuti awaphe.+ 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:25 Nsanja ya Olonda,12/15/2015, tsa. 10
25 Munthu akachimwira mnzake, munthu wina akhoza kumuchonderera kwa Yehova,* koma akachimwira Yehova,+ angamupempherere ndi ndani?” Koma anawo sankamvera bambo awo ndipo tsopano Yehova anali atatsimikiza mtima kuti awaphe.+