1 Samueli 2:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Munthu wa mʼbanja lako amene sindidzamusiyitsa kutumikira paguwa langa lansembe adzachititsa kuti maso ako asamaone komanso adzakuchititsa chisoni. Koma anthu ambiri amʼbanja lako adzaphedwa ndi lupanga.+
33 Munthu wa mʼbanja lako amene sindidzamusiyitsa kutumikira paguwa langa lansembe adzachititsa kuti maso ako asamaone komanso adzakuchititsa chisoni. Koma anthu ambiri amʼbanja lako adzaphedwa ndi lupanga.+