1 Samueli 2:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Koma pali munthu wa m’nyumba yako amene sindidzamuchotsa paguwa langa lansembe kuti achititse maso ako mdima ndi kukufooketsa. Ngakhale zili choncho, ochuluka a m’nyumba yako, anthu adzawapha ndi lupanga.+
33 Koma pali munthu wa m’nyumba yako amene sindidzamuchotsa paguwa langa lansembe kuti achititse maso ako mdima ndi kukufooketsa. Ngakhale zili choncho, ochuluka a m’nyumba yako, anthu adzawapha ndi lupanga.+