2 Samueli 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho mfumu inanyamuka nʼkukakhala pageti. Kenako anthu onse anauzidwa kuti: “Mfumu yakhala pageti.” Ndiyeno anthu anabwera pamene panali mfumuyo. Koma Aisiraeli anali atathawira kunyumba zawo.+
8 Choncho mfumu inanyamuka nʼkukakhala pageti. Kenako anthu onse anauzidwa kuti: “Mfumu yakhala pageti.” Ndiyeno anthu anabwera pamene panali mfumuyo. Koma Aisiraeli anali atathawira kunyumba zawo.+