8 Choncho mfumu inanyamuka ndi kukakhala kuchipata.+ Zitatero uthenga unapita kwa anthu onse kuti: “Mfumu yakhala kuchipata.” Pamenepo anthu onse anayamba kubwera kwa mfumu.
Koma Aisiraeli onse amene anagonjetsedwa, aliyense anathawira kunyumba yake.+