2 Mafumu 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno munthu wa Mulungu woona uja+ anatumiza uthenga kwa mfumu ya Isiraeli, wakuti: “Musadutse pamalo akutiakuti chifukwa Asiriya akupita kumeneko.”
9 Ndiyeno munthu wa Mulungu woona uja+ anatumiza uthenga kwa mfumu ya Isiraeli, wakuti: “Musadutse pamalo akutiakuti chifukwa Asiriya akupita kumeneko.”