2 Mafumu 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako munthu wa Mulungu woona+ uja anatumiza uthenga kwa mfumu ya Isiraeli, wakuti: “Samalani kuti musadutse pamalo akutiakuti+ chifukwa Asiriya akupita kumeneko.”+
9 Kenako munthu wa Mulungu woona+ uja anatumiza uthenga kwa mfumu ya Isiraeli, wakuti: “Samalani kuti musadutse pamalo akutiakuti+ chifukwa Asiriya akupita kumeneko.”+