-
2 Mafumu 6:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Mfumuyo inayankha kuti: “Ngati Yehova sakukuthandiza ndiye ine ndingakuthandize ndi chiyani? Kodi ndingakuthandize ndi zochokera popunthira mbewu, mopondera mphesa kapena moyengera mafuta?”
-