2 Mafumu 6:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Mfumuyo inayankha kuti: “Ngati Yehova sakukuthandiza ndiye ine ndingakuthandize ndi chiyani?+ Kodi ndingakuthandize ndi zochokera popunthira mbewu, mopondera mphesa, kapena moyengera mafuta?”
27 Mfumuyo inayankha kuti: “Ngati Yehova sakukuthandiza ndiye ine ndingakuthandize ndi chiyani?+ Kodi ndingakuthandize ndi zochokera popunthira mbewu, mopondera mphesa, kapena moyengera mafuta?”