-
1 Mbiri 7:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Maaka mkazi wa Makiri anabereka mwana wamwamuna ndipo anamupatsa dzina loti Peresi. Mchimwene wake wa Peresi anali Seresi ndipo ana ake anali Ulamu ndi Rekemu.
-