-
1 Mbiri 7:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Patapita nthawi, Maaka mkazi wa Makiri anabereka mwana wamwamuna ndipo anamupatsa dzina loti Peresi. M’bale wake wa Peresi dzina lake linali Seresi, ndipo ana ake anali Ulamu ndi Rekemu.
-