1 Mbiri 7:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kenako Efuraimu anagona ndi mkazi wake ndipo mkaziyo anatenga pakati nʼkubereka mwana wamwamuna. Koma Efuraimu anapatsa mwanayo dzina lakuti Beriya,* chifukwa mkaziyo anabereka pa nthawi imene tsoka linagwera nyumba ya Efuraimu.
23 Kenako Efuraimu anagona ndi mkazi wake ndipo mkaziyo anatenga pakati nʼkubereka mwana wamwamuna. Koma Efuraimu anapatsa mwanayo dzina lakuti Beriya,* chifukwa mkaziyo anabereka pa nthawi imene tsoka linagwera nyumba ya Efuraimu.