1 Mbiri 7:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kenako Efuraimu anagona ndi mkazi wake, ndipo mkaziyo anatenga pakati+ n’kubereka mwana wamwamuna. Koma Efuraimu anatcha mwanayo dzina lakuti Beriya,* chifukwa mkaziyo anabereka pa nthawi imene tsoka+ linagwera nyumba ya Efuraimu.
23 Kenako Efuraimu anagona ndi mkazi wake, ndipo mkaziyo anatenga pakati+ n’kubereka mwana wamwamuna. Koma Efuraimu anatcha mwanayo dzina lakuti Beriya,* chifukwa mkaziyo anabereka pa nthawi imene tsoka+ linagwera nyumba ya Efuraimu.