2 Mbiri 24:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Nkhani zokhudza ana ake, mauthenga ochuluka omutsutsa+ ndiponso ntchito yokonza* nyumba ya Mulungu woona,+ zinalembedwa mʼBuku la Mafumu. Kenako Amaziya mwana wake anakhala mfumu mʼmalo mwake.
27 Nkhani zokhudza ana ake, mauthenga ochuluka omutsutsa+ ndiponso ntchito yokonza* nyumba ya Mulungu woona,+ zinalembedwa mʼBuku la Mafumu. Kenako Amaziya mwana wake anakhala mfumu mʼmalo mwake.