2 Mbiri 24:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Nkhani zokhudza ana ake, mauthenga ochuluka omutsutsa,+ ndi ntchito yokonzanso maziko+ a nyumba ya Mulungu woona, zinalembedwa m’ndemanga za Buku+ la Mafumu. Kenako Amaziya+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.
27 Nkhani zokhudza ana ake, mauthenga ochuluka omutsutsa,+ ndi ntchito yokonzanso maziko+ a nyumba ya Mulungu woona, zinalembedwa m’ndemanga za Buku+ la Mafumu. Kenako Amaziya+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.