-
2 Mbiri 27:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Yotamu anamenyana ndi mfumu ya Aamoni+ ndipo patapita nthawi anawagonjetsa. Choncho chaka chimenecho Aamoni anamʼpatsa matalente* a siliva 100, tirigu wokwana miyezo 10,000 ya kori* komanso balere wokwana miyezo 10,000 ya kori. Aamoni anamupatsanso zinthu zimenezi mʼchaka chachiwiri ndi chachitatu.+
-