2 Mbiri 27:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye anakhala mfumu ali ndi zaka 25 ndipo analamulira zaka 16 ku Yerusalemu.+