Nehemiya 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Nditangomva mawu amenewa, ndinakhala pansi nʼkuyamba kulira ndipo ndinalira kwa masiku angapo, kusala kudya+ komanso kupemphera kwa Mulungu wakumwamba.
4 Nditangomva mawu amenewa, ndinakhala pansi nʼkuyamba kulira ndipo ndinalira kwa masiku angapo, kusala kudya+ komanso kupemphera kwa Mulungu wakumwamba.