Nehemiya 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno nditangomva mawu amenewa, ndinakhala pansi n’kuyamba kulira. Kwa masiku angapo ndinali kulira, kusala kudya+ ndi kupemphera pamaso pa Mulungu wakumwamba.+
4 Ndiyeno nditangomva mawu amenewa, ndinakhala pansi n’kuyamba kulira. Kwa masiku angapo ndinali kulira, kusala kudya+ ndi kupemphera pamaso pa Mulungu wakumwamba.+