Nehemiya 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Amuna a ku Yeriko+ anamanga kuyambira pamene Eliyasibu ndi abale ake analekezera. Ndipo Zakuri mwana wa Imiri, anapitiriza kuyambira pamene amuna a ku Yeriko analekezera.
2 Amuna a ku Yeriko+ anamanga kuyambira pamene Eliyasibu ndi abale ake analekezera. Ndipo Zakuri mwana wa Imiri, anapitiriza kuyambira pamene amuna a ku Yeriko analekezera.