Nehemiya 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Amuna a ku Yeriko+ nawonso anamanga kuyambira pamene Eliyasibu ndi abale ake analekezera. Kenako, Zakuri mwana wamwamuna wa Imiri, anamanga kuyambira pamene amuna a ku Yeriko analekezera.
2 Amuna a ku Yeriko+ nawonso anamanga kuyambira pamene Eliyasibu ndi abale ake analekezera. Kenako, Zakuri mwana wamwamuna wa Imiri, anamanga kuyambira pamene amuna a ku Yeriko analekezera.